Deuteronomo 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chakudya chimene azikalandira chikakhale chofanana ndi cha ansembe onse,+ kuwonjezera pa zimene walandira atagulitsa cholowa chimene analandira kwa makolo ake.
8 Chakudya chimene azikalandira chikakhale chofanana ndi cha ansembe onse,+ kuwonjezera pa zimene walandira atagulitsa cholowa chimene analandira kwa makolo ake.