Deuteronomo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova Mulungu wanu akadzawonjezera dziko lanu mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu,+ nʼkukupatsani dziko lonse limene analonjeza makolo anu kuti adzawapatsa,+
8 Yehova Mulungu wanu akadzawonjezera dziko lanu mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu,+ nʼkukupatsani dziko lonse limene analonjeza makolo anu kuti adzawapatsa,+