Deuteronomo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukatsala pangʼono kuyamba nkhondo, wansembe azifika pafupi nʼkulankhula ndi anthu.+