-
Deuteronomo 21:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 “Ngati mwapeza munthu wakufa pathengo, mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala lanu, ndipo amene wapha munthuyo sakudziwika,
-