Deuteronomo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 akulu ndi oweruza anu+ azipita kukayeza mtunda kuchokera pamene pali munthu wakufayo kukafika kumizinda yonse yozungulira malo amene munthuyo wapezeka.
2 akulu ndi oweruza anu+ azipita kukayeza mtunda kuchokera pamene pali munthu wakufayo kukafika kumizinda yonse yozungulira malo amene munthuyo wapezeka.