Deuteronomo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akulu a mumzindawo azitenga ngʼombeyo nʼkupita nayo kuchigwa chimene chili* ndi madzi oyenda. Chigwa chimenechi chikhale choti sichinalimidwepo kapena kudzalidwa mbewu. Akafika kumeneko azipha ngʼombe yaingʼonoyo poithyola khosi.+
4 Akulu a mumzindawo azitenga ngʼombeyo nʼkupita nayo kuchigwa chimene chili* ndi madzi oyenda. Chigwa chimenechi chikhale choti sichinalimidwepo kapena kudzalidwa mbewu. Akafika kumeneko azipha ngʼombe yaingʼonoyo poithyola khosi.+