Deuteronomo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngati simukusangalala naye muzimulola kuti achoke+ nʼkupita kulikonse kumene akufuna. Koma simukuyenera kumugulitsa kapena kumuchitira nkhanza, chifukwa mwamuchititsa manyazi.
14 Koma ngati simukusangalala naye muzimulola kuti achoke+ nʼkupita kulikonse kumene akufuna. Koma simukuyenera kumugulitsa kapena kumuchitira nkhanza, chifukwa mwamuchititsa manyazi.