-
Deuteronomo 22:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 ndipo akumuimba mlandu wochita khalidwe loipa ponena kuti: “Ndaona kuti palibe umboni wosonyeza kuti mwana wanuyu anali namwali.” Koma umboni wosonyeza kuti mwana wanga anali namwali ndi uwu.’ Akatero azitambasula chofunda pamaso pa akulu a mzindawo.
-