Deuteronomo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati mwamuna wadetsedwa chifukwa chotulutsa umuna usiku,+ azipita kunja kwa msasa ndipo asamalowenso mumsasamo.
10 Ngati mwamuna wadetsedwa chifukwa chotulutsa umuna usiku,+ azipita kunja kwa msasa ndipo asamalowenso mumsasamo.