Deuteronomo 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno madzulo azisamba ndi madzi ndipo kenako angathe kubwerera kumsasa dzuwa likalowa.+