Deuteronomo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mukalowa mʼmunda wa mpesa wa mnzanu mungathe kudya mphesa mmene mungathere kuti mukhute, koma musamaike zina mʼthumba lanu.+
24 Mukalowa mʼmunda wa mpesa wa mnzanu mungathe kudya mphesa mmene mungathere kuti mukhute, koma musamaike zina mʼthumba lanu.+