-
Deuteronomo 25:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiye ngati mwamunayo sakufuna kukwatira mkazi wamasiye wa mchimwene wakeyo, mkaziyo azipita kwa akulu pageti nʼkuwauza kuti, ‘Mchimwene wa mwamuna wanga wakana kusunga dzina la mchimwene wake mu Isiraeli. Sanavomereze kuchita ukwati wa pachilamu ndi ine.’
-