Deuteronomo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo tsiku limene muwoloke Yorodano nʼkulowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, mukaimike miyala ikuluikulu nʼkuipanga pulasitala.*+
2 Ndipo tsiku limene muwoloke Yorodano nʼkulowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, mukaimike miyala ikuluikulu nʼkuipanga pulasitala.*+