Deuteronomo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukawoloka Yorodano, mukaimike miyala imeneyi paphiri la Ebala,+ ndipo mukaipange pulasitala,* mogwirizana ndi zimene ndikukulamulani lero.
4 Mukawoloka Yorodano, mukaimike miyala imeneyi paphiri la Ebala,+ ndipo mukaipange pulasitala,* mogwirizana ndi zimene ndikukulamulani lero.