Deuteronomo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Mukamveradi mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsani lero, Yehova Mulungu wanu adzakukwezani ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:1 Nsanja ya Olonda,12/15/1995, ptsa. 26-27
28 “Mukamveradi mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsani lero, Yehova Mulungu wanu adzakukwezani ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+