Deuteronomo 28:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Iye adzakukongozani zinthu koma inuyo simudzatha kumukongoza.+ Iye adzakhala mutu koma inuyo mudzakhala mchira.+
44 Iye adzakukongozani zinthu koma inuyo simudzatha kumukongoza.+ Iye adzakhala mutu koma inuyo mudzakhala mchira.+