Deuteronomo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu ndipo apitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+
8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu ndipo apitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+