Deuteronomo 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo amene akukhala mʼmizinda yanu,* kuti amvetsere komanso kuti aphunzire zokhudza Yehova Mulungu wanu, kuti azimuopa ndiponso kuti azitsatira mosamala mawu onse a mʼChilamulo ichi. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:12 Nsanja ya Olonda,4/15/2010, tsa. 39/15/2004, tsa. 273/15/2000, tsa. 17
12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo amene akukhala mʼmizinda yanu,* kuti amvetsere komanso kuti aphunzire zokhudza Yehova Mulungu wanu, kuti azimuopa ndiponso kuti azitsatira mosamala mawu onse a mʼChilamulo ichi.