Deuteronomo 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzalefuka ndi njala+Ndipo adzavutika ndi kutentha thupi koopsa komanso adzawonongedwa nʼkutheratu.+ Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali+Komanso njoka zapoizoni za mʼfumbi.
24 Adzalefuka ndi njala+Ndipo adzavutika ndi kutentha thupi koopsa komanso adzawonongedwa nʼkutheratu.+ Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali+Komanso njoka zapoizoni za mʼfumbi.