11 “Pitani mumsasa wonsewu, mukauze anthu kuti, ‘Konzekani ndipo mupezeretu zinthu zonse zofunikira, chifukwa pakapita masiku atatu muwoloka Yorodano nʼkulowa mʼdzikolo kuti mukalitenge, dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu.’”+