-
Yoswa 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mfumu ya Yeriko itamva zimenezi, inatumiza anthu kukauza Rahabi kuti: “Tulutsa amuna amene abwera kuno ndipo ali mʼnyumba mwako, chifukwa abwera kudzafufuza dziko lonseli.”
-