Yoswa 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo anathamangira amuna aja cha kowolokera mtsinje wa Yorodano.+ Ndipo atangotuluka pageti la mzinda, nthawi yomweyo getilo linatsekedwa.
7 Anthuwo anathamangira amuna aja cha kowolokera mtsinje wa Yorodano.+ Ndipo atangotuluka pageti la mzinda, nthawi yomweyo getilo linatsekedwa.