Yoswa 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mayiyo anawapatsa chingwe ndipo iwo anatulukira pawindo pogwiritsa ntchito chingwecho, chifukwa mpanda wa mzindawo unalinso khoma la nyumba yake. Tingoti khoma la nyumba yakeyo linali mbali ya mpandawo.+
15 Kenako mayiyo anawapatsa chingwe ndipo iwo anatulukira pawindo pogwiritsa ntchito chingwecho, chifukwa mpanda wa mzindawo unalinso khoma la nyumba yake. Tingoti khoma la nyumba yakeyo linali mbali ya mpandawo.+