-
Yoswa 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Choncho amuna aja anapita kumapiri ndipo anakhala kumeneko masiku atatu mpaka anthu owasakawo atabwerera. Owasakawo anali atawafunafuna mumsewu uliwonse, koma osawapeza.
-