Yoswa 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼmamawa kutacha, Yoswa ndi Aisiraeli* onse ananyamuka ku Sitimu+ nʼkuyenda kukafika kumtsinje wa Yorodano. Iwo anagona kumeneko asanawoloke.
3 Mʼmamawa kutacha, Yoswa ndi Aisiraeli* onse ananyamuka ku Sitimu+ nʼkuyenda kukafika kumtsinje wa Yorodano. Iwo anagona kumeneko asanawoloke.