Yoswa 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndipo anauza anthuwo kuti: “Mukangoona likasa la pangano la Yehova Mulungu wanu litanyamulidwa ndi Alevi omwe ndi ansembe,+ musamuke pamalo panu nʼkuyamba kulitsatira,
3 ndipo anauza anthuwo kuti: “Mukangoona likasa la pangano la Yehova Mulungu wanu litanyamulidwa ndi Alevi omwe ndi ansembe,+ musamuke pamalo panu nʼkuyamba kulitsatira,