Yoswa 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 koma musaliyandikire. Pakati pa inu ndi likasalo pakhale mtunda wokwana mikono pafupifupi 2,000.* Mukatero mudzadziwa koyenera kupita, chifukwa kumeneko simunayambe mwapitako.”
4 koma musaliyandikire. Pakati pa inu ndi likasalo pakhale mtunda wokwana mikono pafupifupi 2,000.* Mukatero mudzadziwa koyenera kupita, chifukwa kumeneko simunayambe mwapitako.”