Yoswa 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Yoswa anauza ansembe kuti: “Nyamulani likasa+ la pangano ndipo muziyenda patsogolo pa anthuwa.” Choncho ansembewo ananyamula likasa la panganolo nʼkumayenda patsogolo pa anthuwo.
6 Kenako Yoswa anauza ansembe kuti: “Nyamulani likasa+ la pangano ndipo muziyenda patsogolo pa anthuwa.” Choncho ansembewo ananyamula likasa la panganolo nʼkumayenda patsogolo pa anthuwo.