Yoswa 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano tengani amuna 12 mʼmafuko a Isiraeli, mwamuna mmodzi pafuko lililonse.+