Yoswa 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene zichitike nʼzakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda mʼmadzi a mumtsinje wa Yorodano, madzi ochokera kumtunda aima nʼkukhala ngati khoma.”+
13 Zimene zichitike nʼzakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda mʼmadzi a mumtsinje wa Yorodano, madzi ochokera kumtunda aima nʼkukhala ngati khoma.”+