Yoswa 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho anthuwo anachotsa mahema awo, nʼkunyamuka kuti awoloke Yorodano, ndipo ansembe onyamula likasa+ la pangano anali patsogolo pawo.
14 Choncho anthuwo anachotsa mahema awo, nʼkunyamuka kuti awoloke Yorodano, ndipo ansembe onyamula likasa+ la pangano anali patsogolo pawo.