Yoswa 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onyamula Likasawo atangofika pamtsinje wa Yorodano, nʼkuponda madzi a mʼmphepete mwake (mtsinje wa Yorodano unkasefukira+ nyengo yonse yokolola), Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Nsanja ya Olonda,12/1/2004, tsa. 812/15/1986, tsa. 15
15 Onyamula Likasawo atangofika pamtsinje wa Yorodano, nʼkuponda madzi a mʼmphepete mwake (mtsinje wa Yorodano unkasefukira+ nyengo yonse yokolola),