-
Yoswa 4:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndipo anawauza kuti: “Dutsani kutsogolo kwa Likasa la Yehova Mulungu wanu, mukafike pakati pa mtsinje wa Yorodano. Aliyense akanyamule mwala umodzi paphewa pake, mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a Aisiraeli.
-