Yoswa 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso Yoswa anatenga miyala 12 nʼkuisanja pakati pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe onyamula likasa la pangano anaima.+ Miyalayo ilipo mpaka lero. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda,12/15/1986, ptsa. 16-17
9 Komanso Yoswa anatenga miyala 12 nʼkuisanja pakati pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe onyamula likasa la pangano anaima.+ Miyalayo ilipo mpaka lero.