-
Yoswa 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ansembe onyamula Likasawo, anaimabe pakati pa mtsinje wa Yorodano, mpaka zonse zimene Yehova analamula Yoswa kuti auze anthuwo zitachitika, mogwirizana ndi zonse zimene Mose analamula Yoswa. Ansembewo ali chiimire choncho, anthuwo anawoloka mtsinjewo mofulumira.
-