Yoswa 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu onse atangotha kuwoloka, Likasa la Yehova linawoloka litanyamulidwa ndi ansembewo, anthu onsewo akuona.+
11 Anthu onse atangotha kuwoloka, Likasa la Yehova linawoloka litanyamulidwa ndi ansembewo, anthu onsewo akuona.+