Yoswa 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe onyamula likasa+ la pangano la Yehova atachoka pakati pa mtsinje wa Yorodano, komanso mapazi awo atangoponda pamtunda, madzi a mtsinjewo anayambanso kuyenda ndipo anasefukira mbali zonse+ ngati poyamba.
18 Ansembe onyamula likasa+ la pangano la Yehova atachoka pakati pa mtsinje wa Yorodano, komanso mapazi awo atangoponda pamtunda, madzi a mtsinjewo anayambanso kuyenda ndipo anasefukira mbali zonse+ ngati poyamba.