Yoswa 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yoswa anawadula chifukwa chakuti amuna onse amene anatuluka mu Iguputo, onse otha kupita kunkhondo,* anali atafera mʼchipululu pa ulendo wochokera ku Iguputo.+
4 Yoswa anawadula chifukwa chakuti amuna onse amene anatuluka mu Iguputo, onse otha kupita kunkhondo,* anali atafera mʼchipululu pa ulendo wochokera ku Iguputo.+