-
Yoswa 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Anthu onse amene anachoka ku Iguputo anali odulidwa. Koma onse amene anabadwira mʼchipululu pa ulendo wochokera ku Iguputo, anali asanadulidwe.
-