Yoswa 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye analowetsa mʼdzikomo ana awo mʼmalo mwa iwowo.+ Ana amenewa Yoswa anawadula, chifukwa sanadulidwe pa nthawi imene anali pa ulendo.
7 Iye analowetsa mʼdzikomo ana awo mʼmalo mwa iwowo.+ Ana amenewa Yoswa anawadula, chifukwa sanadulidwe pa nthawi imene anali pa ulendo.