Yoswa 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachititsa kuti Aiguputo asamakunyozeninso.”* Choncho malowo amawatchula kuti Giligala,*+ mpaka lero.
9 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndachititsa kuti Aiguputo asamakunyozeninso.”* Choncho malowo amawatchula kuti Giligala,*+ mpaka lero.