Yoswa 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yoswa mwana wa Nuni anaitana ansembe nʼkuwauza kuti: “Nyamulani likasa la pangano, ndipo ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa la Yehovalo. Ansembewo atenge malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo.”+
6 Choncho Yoswa mwana wa Nuni anaitana ansembe nʼkuwauza kuti: “Nyamulani likasa la pangano, ndipo ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa la Yehovalo. Ansembewo atenge malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo.”+