Yoswa 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anauzanso asilikali kuti: “Nyamukani, mukagube kuzungulira mzindawo. Gulu la asilikali onyamula zida zankhondo+ likhale patsogolo pa Likasa la Yehova.”
7 Anauzanso asilikali kuti: “Nyamukani, mukagube kuzungulira mzindawo. Gulu la asilikali onyamula zida zankhondo+ likhale patsogolo pa Likasa la Yehova.”