-
Yoswa 6:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Monga Yoswa ananenera, ansembe 7 ananyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa pamaso pa Yehova. Iwo anatsogola akuliza malipengawo, ndipo likasa la pangano la Yehova linkabwera pambuyo pawo.
-