-
Yoswa 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Yoswa analamula asilikaliwo kuti: “Musafuule kapena kulankhula kanthu, ndipo pakamwa panu pasatuluke mawu alionse mpaka tsiku limene ndidzakuuzani kuti, ‘Fuulani!’ Pamenepo mudzafuule.”
-