-
Yoswa 6:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho iye atalamula, Likasa la Yehova linazungulira mzindawo kamodzi, asilikaliwo akuguba nalo. Kenako iwo anabwerera kumsasa ndipo anakhala kumeneko usiku wonse.
-