-
Yoswa 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ansembe 7 onyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa, omwe ankakhala patsogolo pa Likasa la Yehova, ankayenda akuliza malipenga mosalekeza. Patsogolo pawo panali gulu la asilikali onyamula zida, ndipo pambuyo pa Likasa la Yehova pankabwera asilikali ena, uku malipenga akulira mosalekeza.
-