Yoswa 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anagubanso kuzungulira mzindawo kamodzi pa tsiku lachiwirili ndipo atamaliza anabwerera kumsasa. Anachita zimenezi kwa masiku 6.+
14 Iwo anagubanso kuzungulira mzindawo kamodzi pa tsiku lachiwirili ndipo atamaliza anabwerera kumsasa. Anachita zimenezi kwa masiku 6.+