Yoswa 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la 7, anadzuka mʼmamawa kwambiri ndipo anaguba kuzungulira mzindawo ngati mmene ankachitira. Pa tsikuli anazungulira mzindawo maulendo 7.+
15 Pa tsiku la 7, anadzuka mʼmamawa kwambiri ndipo anaguba kuzungulira mzindawo ngati mmene ankachitira. Pa tsikuli anazungulira mzindawo maulendo 7.+