Yoswa 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akanani ndi anthu onse a mʼdzikoli adzamva zimenezi, ndipo adzabwera nʼkufafaniza dzina lathu padziko lapansi. Ndiye mudzateteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+
9 Akanani ndi anthu onse a mʼdzikoli adzamva zimenezi, ndipo adzabwera nʼkufafaniza dzina lathu padziko lapansi. Ndiye mudzateteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+